Symon & Kendall – Kumadya (Official Music Video)
Symon & Kendall – Kumadya (Official Music Video)
Mafumu azakudya, kulangiza azibambo kuti azidya!!!
source
Reviews
0 %
This is a demo advert, you can use simple text, HTML image or any Ad Service JavaScript code. If you're inserting HTML or JS code make sure editor is switched to 'Text' mode.
😅😅😅wow😮
❤
thats nice
Mpaka pakati pausiku kudzukilira kutenthetsa mbwanda aaaa ena akuonjeza anyway kumadyaaaa😂😂🔥🔥
Pyooooooo❤❤❤🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kumadya
Kuno ena sakudya angokhalira mowa
😂😂😂😂😂😂Moto kt bu🔥 bu🔥 bu 🔥
sanalakwe ndiufuru wake kusankha chipani chomwe akufu
Nza akulu akulu izi😂😂😂😂
Eya anachita bwino ndi ufulu wake
🤣😂🤣🇱🇾🔥🇲🇿
😂😂😂😂 Phwedo amuyenda pansi😅
Azimayi mzitimvetsaaa 😂😂😂😂🎉🎉🎉 nzinziri olo muli inu mkadatanii
I am a legend but i dont understand
Komano nsima yonseyo anapanga nayo chani tiziti anataya???coz ndizabodza kuti nsima imeneyo inadyedwa yonse 😮😮
Fertiliser mpaka k100000 mkumayimba nyimbo zautsiruzo chibwana eti Dpp my vote
Komano akutanthawuzatu kudya😅
Zikumatha ngat zikuyamba❤
Aphwedo mwawaphikisa ulele 😅😅😅 amamenyatu uyi 😂😂😂
Matimangatu mchikwatu osanama nyimbo iyi😅😅😅
Symon & Kendall, back at it again with another amazing banger! Love these guys. Every song is always a hit! 🇲🇼 🇲🇼 🇲🇼
😂😂😂 Mbambande azibambo
Kod phwedo.akuyendera it makamaka😂😂😂😂
Tili pano🔥🔥
Great song mwana mkazi
Kkkkk 😂😂😂 what type of food are you talking about?
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🙆koma ndiye mwanipanga achimwene kkkkkk
more fire 🔥
Tiyeni tizidyani mmanyumbamu kkkk
Wavala delesi ya blue latimaluwa akumavina mere wakusogolo pa Namba 2 kumanja, ndi nkazidi koma? Eeeeeeee,akunjonjola ngati nkhwali. Ndimangoona pompo nthawi zonse
memo mu will barroiw kkkk
Iwe ndi dolo aise, osachimvela chitsilu chimwendo banda wa mutu ngati bus 🚍 mbuzi yeni yeni
Screen
Kkkk
Ati
Kumadyat
Osamagoona
Km
Pang, ono
PokhA
,, km
Amaitha