A Malawi Sanakwiye Aliyense Opanga Ma Demo Watumidwa Ndi DPP – Ken Msonda


A Malawi Sanakwiye Aliyense Opanga Ma Demo Watumidwa Ndi DPP – Ken Msonda


On Nyasa VoiceBox, Ken Msonda says Malawians are not unhappy with the government led by president Chakwera. Malawians understand that the current economic situation is not isolated to Malawi but the global economy is not doing well. So if you see anyone protesting, just know that they are sponsored by DPP because DPP realise they cannot win the…

source

Leave your comment

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Prove your humanity: 1   +   7   =  

32 Comments

  1. Peter angatume anthu kugenda or ku chita mademo ku Lilongwe? Mavendor achigawo cha pakati angatumidwe ndi DPP? M'sonda wasowa cholankhura eti?
    Dzikomo Chakwela wabvomeleza kuti tisankhe wina. Manyadzi agwila m'sonda.

  2. Uyu pofuniadzagendedwe nsonda akapezeka pabwino tinchailire guys.koma apezeka basi oloabisale tidzamuthidzimula nawo mwala ameneyu sakuwudziwa.amfunse nzake chimwendo ndi kashort kazamalondako

  3. Kkkk iwe nsonda usapangise amalawi mitima ikweleletu kwambili pano ndiyokwela kale.iwe ngoszetsa chisokonezo dziko.chilichonse you point finger to DPP.iwe dpp ndalama zowapanga sponsor gululonse lija angalipeze kut?mesa mwaba ndinu a mcp ma $ dollars.imagine mene ma vendor apanga zioneselo mwawatulusa ma 💸 munawabisawo.lero pansika palibwino ndalama ikutsika agalu okuba inu.munatibisila ndalama zathu.sindalama zanu ayi anyapapinu mumapempha mudzina la amalawi kunjako koma sizimatifikila mumangoba agalu achabe chabe Eni ndalamafe kumavutika akhakhakha.